2 Samueli 23:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipongwazi zitatuzo zinapyola khamu la Afilisti, nizitunga madzi m'citsime ca ku Betelehemu, ca pa cipataco, nawatenga, nafika nao kwa Davide; koma iye sanafuna kumwako, koma anawathira pansi kwa Yehova.

2 Samueli 23

2 Samueli 23:14-25