2 Samueli 12:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano wafa, ndidzasaliranjinso kudya? Kodi ndikhoza kumbweza? Ine ndidzamuka kuli iye, koma iye sadzabweranso kwa ine.

2 Samueli 12

2 Samueli 12:16-24