2 Samueli 12:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Pamene mwanayo akali ndi moyo, ndinasala kudya ndi kulira, pakuti ndinati, Adziwa ndani kapena Yehova adzandicitira cifundo kuti mwanayo akhale ndi moyo.

2 Samueli 12

2 Samueli 12:14-27