2 Samueli 12:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anyamata ace ananena naye, Ici mwacita nciani? Mwanayo akali moyo, munasala kudya ndi kumlira, koma pakufa mwanayo munyamuka ndi kudya,

2 Samueli 12

2 Samueli 12:12-28