2 Samueli 10:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Yoabu ndi anthu amene anali naye anayandikira kuponyana nkhondo ndi Aaramu. Ndipo iwowa anathawa pamaso pace.

2 Samueli 10

2 Samueli 10:3-19