2 Samueli 10:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene ana a Amoni anaona kuti Aaramu anathawa, iwonso anathawa pamaso pa Abisai, nalowa m'mudzimo. Ndipo Yoabu anabwera kucokera kwa ana a Amoni, nafika ku Yerusalemu.

2 Samueli 10

2 Samueli 10:10-19