2 Mbiri 31:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anacita Hezekiya mwa Yuda lonse nacita cokoma, ndi coyenera, ndi cokhulupirika, pamaso pa Yehova Mulungu wace.

2 Mbiri 31

2 Mbiri 31:10-21