2 Mbiri 31:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

panalinso amuna mwa ana a Aroni ansembe, okhala m'minda ya kubusa kwa midzi yao, m'mudzi uli wonse, ochulidwa maina ao, agawire amuna onse mwa ansembe, ndi onse mwa Alevi, oyesedwa mwa cibadwidwe magawo ao.

2 Mbiri 31

2 Mbiri 31:12-21