2 Mbiri 31:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'nchito iri yonse anaiyamba m'utumiki wa nyumba ya Mulungu, ndi m'cilamulo, ndi m'mauzo, kufuna Mulungu wace, anacita ndi mtima wace wonse, nalemerera nayo.

2 Mbiri 31

2 Mbiri 31:14-21