2 Mbiri 29:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti analakwa makolo athu, nacita coipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu, namsiya, natembenuza nkhope zao osapenya cokhalamo Yehova, namfulatira.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:1-7