2 Mbiri 29:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena nao, Ndimvereni, Alevi inu, dzipatuleni, nimupatule nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu, ndi kucotsa zoipsa m'malo opatulika.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:1-11