2 Mbiri 29:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anatsekanso pa khomo la likole, nazima nyalizo, osafukizanso zonunkhira kapena kupereka nsembe zopsereza m'malo opatulika kwa Mulungu wa Israyeli.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:1-15