2 Mbiri 29:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe analowa m'kati mwace mwa nyumba ya Yehova kuiyeretsa, naturutsira ku bwalo la nyumba ya Yehova zoipsa zonse anazipeza m'Kacisi wa Yehova. Nazilandira Alevi, kuziturutsira kunja ku mtsinje wa Kedroni.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:13-19