2 Mbiri 29:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anayamba tsono kuipatula tsiku loyamba la mwezi woyamba, nafikira ku likole la Yehova tsiku lacisanu ndi citatu la mwezi, naipatula nyumba ya Yehova m'masiku asanu ndi atatu; natsiriza tsiku lakhumi ndi cisanu ndi cimodzi.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:9-19