2 Mbiri 29:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamemeza abale ao, nadzipatula, nalowa monga adawauza mfumu mwa mau a Yehova, kuyeretsa nyumba ya Yehova.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:11-22