2 Mbiri 25:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Amaziya anati kwa munthu wa Mulungu, Koma nanga titani nao matalente zana limodzi ndinapatsa ankhondo a Israyeli? Nati munthu wa Mulungu, Yehova ali nazo zoposa izi kukupatsani.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:3-13