2 Mbiri 25:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Amaziya anawapambutsa, ndiwo ankhondo anamdzera kucokera ku Efraimu, amuke kwao; potero adapsa mtima kwambiri pa Yuda, nabwera kwao ndi kutentha mtima.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:1-20