2 Mbiri 25:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati mumuka, citani, limbikani kunkhondo, Mulungu adzakugwetsani pamaso pa adani; pakuti Mulungu ali nayo mphamvu yakuthandiza ndi yakugwetsa.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:7-18