2 Mbiri 25:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anamdzera munthu wa Mulungu, kuti, Mfumu, khamu la nkhondo la Israyeli lisapite nanu; pakuti Yehova sakhala ndi Israyeli, sakhala ndi ana onse a Efraimu.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:1-14