2 Mbiri 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Analemberanso ngwazi zamphamvu za m'Israyeli zikwi zana limodzi, kuwalipira matalente a siliva zana limodzi.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:1-14