2 Mbiri 25:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atafika Amaziya atatha kuwapha Aedomu, ndi kubwera nayo milungu ya ana a Seiri, anaiika ikhale milungu yace, naigwadira, naifukizira,

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:7-23