2 Mbiri 25:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma amuna a nkhondo amene Amaziya anawabwereretsa, kuti asamuke naye kunkhondo, anagwera midzi ya Yuda kuyambira Samariya kufikira Betihoroni, nakantha a iwowa zikwi zitatu, nalanda zofunkha zambiri.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:6-16