2 Mbiri 25:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mkwiyo wa Mulungu unayakira Amaziya, ndipo anamtumira mneneri amene anati, Mwafuniranji milungu ya anthu imene siinalanditsa anthu ao m'dzanja lanu?

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:7-21