2 Mbiri 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nayenda m'njira ya mafumu a Israyeli, umo anacitira nyumba ya Ahabu; pakuti mwana wamkazi wa Ahabu anali mkazi wace; ndipo anacita coipa pamaso pa Yehova.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:1-14