2 Mbiri 21:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova sanafuna kuononga nyumba ya Davide cifukwa ca pangano adalicita ndi Davide, ndi monga adalonjeza kumpatsa iye ndi ana ace nyali nthawi zonse.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:2-9