2 Mbiri 21:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehoramu anali wa zaka makumi atatu mphambu ziwiri polowa ufumu wace, nacita ufumu m'Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:1-9