2 Mbiri 20:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo poyamba iwo kuyimba, ndi kulemekeza Yehova, anaika olalira alalire Aamoni, Amoabu, ndi a m'phiri la Seiri, akudzera Ayuda; ndipo anawakantha.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:16-30