2 Mbiri 20:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atafunsana ndi anthu, anaika oyimbira Yehova, ndi kulemekeza ciyero cokometsetsa, pakuturuka iwo kutsogolera khamu la nkhondo, ndi kuti, Yamikani Yehova, pakuti cifundo cace cikhala cosatha.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:11-25