2 Mbiri 20:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ana a Amoni, ndi a Moabu, anaukira okhala m'phiri la Seiri, kuwapha ndi kuwaononga psiti; ndipo atatha okhala m'Seiri, anasandulikirana kuonongana.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:16-32