2 Mbiri 16:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti maso a Yehova ayang'ana uko ndi uko m'dziko lonse lapansi, kudzionetsera wamphamvu kwa iwo amene mtima wao uli wangwiro ndi Iye. Mwacita copusa m'menemo; pakuti kuyambira tsopano mudzaona nkhondo.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:3-14