2 Mbiri 16:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Asa anakwiya naye mlauliyo, namuika m'kaidi; pakuti adapsa mtima naye cifukwa ca ici. Nthawi yomweyi Asa anasautsa anthu ena.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:6-14