2 Mbiri 16:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga Akusi ndi Alubi, sanakhala khamu lalikurukuru, ndi magareta ndi apakavalo ambirimbiri, koma muja munatama Yehova anawapereka m'dzanja mwanu?

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:3-14