2 Mbiri 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Asa anaturutsa siliva ndi golidi ku cuma ca nyumba ya Yehova, ndi ca nyumba ya mfumu; nazitumiza kwa Benihadadi mfumu ya Aramu, yokhala ku Damasiko, ndi kuti,

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:1-4