2 Mbiri 16:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi cimodzi ca Asa, Basa mfumu ya Israyeli anakwera kulimbana ndi Yuda, namangitsa Rama, kuwaletsa anthu asaturuke kapena kulowa kwa Asa mfumu ya Yuda.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:1-4