2 Mbiri 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakhale pangano pakati pa ine ndi inu, monga pakati pa atate wange ndi atate wanu; taonani, ndakutumizirani siliva ndi golidi; mukani, pasulani pangano lanu ndi Basa mfumu ya Israyeli, kuti andicokere.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:1-10