2 Mbiri 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamsonkhanira amuna acabe, anthu opanda pace, ndiwo anadzilimbikitsa kutsutsana naye Rehabiamu mwana wa Solomo, muja Rehabiamu anali mnyamata ndi woolowa mtima, wosakhoza kuwalaka.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:2-8