2 Mbiri 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, mukuti mudzilimbikitse kutsutsana nao ufumu wa Yehova m'dzanja la ana a Davide; ndinu aunyinji ambiri, ndi pamodzi nanu ana a ng'ombe agolidi adawapanga Yerobiamu akhale milungu yanu.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:1-13