2 Mafumu 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacita iye zoongoka pamaso pa Yehova, nayenda m'njira yonse ya Davide kholo lace, osapambukira ku dzanja lamanja kapena kulamanzere.

2 Mafumu 22

2 Mafumu 22:1-4