2 Mafumu 22:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca Yosiya, mfumuyi inatuma Safani mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu, mlembi, ku nyumba ya Yehova, ndi kuti,

2 Mafumu 22

2 Mafumu 22:1-7