2 Mafumu 22:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu cimodzi m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndi Yedida mwana wa Adaya wa ku Bozikati.

2 Mafumu 22

2 Mafumu 22:1-8