2 Mafumu 18:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakutha pace pa zaka zitatu anaulanda, ndico caka cacisanu ndi cimodzi ca Hezekiya, ndico caka cacisanu ndi cinai ca Hoseya mfumu ya Israyeli analanda Samariya.

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:4-20