2 Mafumu 18:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali caka cacinai ca mfumu Hezekiya, ndico caka cacisanu ndi ciwiri ca Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israyeli Salimanezeri mfumu ya Asuri anakwerera Samariya, naumangira misasa.

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:4-12