2 Mafumu 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Asuri anacotsa Aisrayeli kumka nao ku Asuri, nawakhalitsa m'Hala, ndi m'Habori, ku mtsinje wa Gozani, ndi m'midzi ya Amedi;

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:8-20