2 Mafumu 16:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nagona Ahazi ndi makolo ace, namuika ndi makolo ace m'mudzi wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwace Hezekiya mwana wace.

2 Mafumu 16

2 Mafumu 16:12-20