2 Mafumu 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka cakhumi ndi ziwiri ca Ahazi mfumu ya Yuda Hoseya mwana wa Ela analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka zisanu ndi zinai.

2 Mafumu 17

2 Mafumu 17:1-11