2 Mafumu 15:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacita coipa pamaso pa Yehova masiku ace onse, osaleka zolakwa za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:11-27