2 Mafumu 15:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Puli mfumu ya Asuri anadza kudzamenyana ndi dziko, koma Menahemu anampatsa Puli matalente a siliva cikwi cimodzi; kuti dzanja lace likhale naye kukhazikitsa ufumu m'dzanja lace.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:10-29