2 Mafumu 15:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi zinai ca Azariya mfumu ya Yuda, Menahemu mwana wa Gadi analowa ufumu wace wa Israyeti, nakhala mfumu zaka khumi m'Samariya.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:8-21