2 Mafumu 15:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Menahemu anakantha Tifisa, ndi onse anali m'mwemo, ndi malire ace kuyambira ku Tiriza; popeza sanamtsegulira pacipata; anaukantha, natumbula akazi onse a pakati okhala m'mwemo.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:7-18