2 Mafumu 15:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa ndi mau a Yehova anawanena ndi Yehu, ndi kuti, Ana ako kufikira mbadwo wacinai adzakhala pa mpando wacifumu wa Israyeli. Ndipo kunatero momwemo.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:7-14